Galatians 3:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja ponena za Abrahamu Malembo akuti, “Iye adaakhulupirira Mulungu, motero Mulungu adamuwona kuti ngwolungama.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga Abrahamu anakhulupirira Mulungu, ndipo kunawerengedwa kwa iye chilungamo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchimodzimodzinso Abrahamu, “Iye anakhulupirira Mulungu, ndipo Mulungu anamutenga kukhala wolungama.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga Abrahamu anakhulupirira Mulungu, ndipo kunawerengedwa kwa iye cilungamo,