Galatians 3:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muzindikire tsono kuti ndi anthu amene amakhulupirira omwe ali ana enieni a Abrahamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chotero zindikirani kuti iwo a chikhulupiriro ndiwo ana a Abrahamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono zindikirani kuti amene akhulupirira, ndi ana a Abrahamu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cotero zindikirani kuti iwo a cikhulupiriro ndiwo ana a Abrahamu.