Galatians 4:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikuwopa kuti mwinatu ntchito zanga zonse pakati panu ndidazigwira pachabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiopera inu, kuti kapena ndadzivutitsa ndi inu chabe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikuopa kuti mwina ntchito zanga pa inu ndinagwira pachabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiopera inu, kuti kapena odadzibvutitsa ndi inu cabe.