Galatians 4:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga mukudziŵa, pamene ndidayamba kukulalikirani Uthenga Wabwino, ndinkadwala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma mudziwa kuti m'kufooka kwa thupi ndinakulalikirani Uthenga Wabwino poyamba:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga inu mukudziwa ndinkakulalikirani Uthenga Wabwino ndili wofowoka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma mudziwa kuti m'kufoka kwa thupi ndinakulalikirani Uthenga Wabwino poyamba: