Galatians 4:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga chimwemwe chanu chija chili kuti tsopano? Ndikukuchitirani umboni kuti nthaŵi imene ija, kukadatheka, mukadakolowola maso anu nkundipatsa ineyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo thamo lanu lili kuti? Pakuti ndikuchitirani inu umboni, kuti, kukadatheka, mukadakolowola maso anu ndi kundipatsa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi chimwemwe chanu chonse chija chili kuti? Ine nditha kuchitira umboni kuti, ngati kukanatheka, inu mukanakolowola maso anu ndi kundipatsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo thamo lanu liri kuti? Pakuti ndikucitirani inu umboni, kuti, kukadatheka, mukadakolowola maso anu ndi kundipatsa ine.