Galatians 4:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwabwino nkumachita changu pa chinthu chabwino masiku onse, osati pokhapokha pamene ndili pamodzi nanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma nkwabwino kuchita changu m'zabwino nthawi zonse, si pokhapokha pokhala nanu pamodzi ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼkwabwino kuchita changu, ngati cholingacho chili chabwino ndi kukhala otero nthawi zonse osati pokhapo pamene ine ndili ndi inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma nkwabwino kucita cangu m'zabwino nthawi zonse, si pokha pokha pokhala nanu pamodzi ine.