Galatians 4:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikadakonda nditakhala nanu tsopano. Apo kapena ndikadasintha mau anga, chifukwa mwandithetsa nzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma mwenzi nditakhala nanu tsopano, ndi kusintha mau anga; chifukwa ndisinkhasinkha nanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ine ndikanakonda ndikanakhala nanu tsopano kuti ndisinthe mawu anga, chifukwa ndathedwa nanu nzeru.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma mwenzi nditakhala nanu tsopano, ndi kusintha mau anga; cifukwa ndisinkhasinkha nanu.