Galatians 4:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono inu abale, ndinu ana a Mulungu chifukwa cha lonjezo lake, monga Isaki.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ife, abale, monga Isaki, tili ana a lonjezano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono inu abale, ndinu ana alonjezo ngati Isake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ife, abale, monga Isake, tiri ana a lonjezano.