Galatians 5:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati muyamba kulumana ndi kukadzulana, muchenjere kuti mungaonongane kotheratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati mulumana ndi kudyana, chenjerani mungaonongane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mupitiriza kulumana ndi kukhadzulana, samalani kuti mungawonongane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati mulumana ndi kudyana, cenjerani mungaonongane.