Galatians 5:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kukopeka kwanu kumeneku sikuchokera kwa Mulungu amene amakuitanani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kukopa kumene sikuchokera kwa Iye anakuitanani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kukopeka kwanu kumeneku sikuchokera kwa Iye amene anakuyitanani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kukopa kumene sikucokera kwa iye anakuitanani.