Galatians 6:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati munthu adziyesa kanthu, pamene chikhalirecho sali kanthu konse, amangodzinyenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ngati wina ayesa ali kanthu pokhala ali chabe, adzinyenga yekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati wina adziyesa kanthu pamene iyeyo sali kanthu konse, akudzinamiza yekha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ngati wina ayesa ali kanthu pokhala ali cabe, adzinyenga yekha.