Genesis 10:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kanani adabereka mwana wake wachisamba dzina lake Sidoni, ndipo adaberekanso Heti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Kanani anabala Sidoni woyamba wake, ndi Heti:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kanaani anabereka mwana wake wachisamba, Sidoni, ndipo anaberekanso Ahiti;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Kanani anabala Sidoni woyamba wace, ndi Heti: