Genesis 10:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Semu ndiye kholo la ana onse a Eberi, ndiponso ndiye mkulu wake wa Yafeti. Iyeyu anali ndi ana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso kwa Semu atate wa ana onse a Eberi, mkulu wa Yafeti, kwa iye kunabadwa ana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Semu amene anali mkulu wake wa Yafeti nayenso anabereka nakhala kholo la Eberi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso kwa Semu atate wa ana onse a Ebere, mkuru wa Yafeti, kwa iye kunabadwa ana.