Genesis 10:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko limene ankakhalamo lidayambira ku Mesa kumaloŵa ku Sefari ku mapiri chakuvuma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwao kunayamba pa Mesa pakunka ku Sefari phiri la kum'mawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chigawo chimene ankakhala chinayambira ku Mesa mpaka ku Seferi, ku dera la mapiri chakummawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwao kunayamba pa Mesa pakunka ku Sefere phiri la kum'mawa.