Genesis 10:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwoŵa ndiwo anali makolo a onse amene ankakhala m'mbali mwa nyanja, ndi pa zilumba zam'nyanja. Ameneŵa ndiwo ana a Yafeti. Mafuko ao anali osiyanasiyana, ndipo ankakhala m'maiko osiyanasiyana. Fuko lililonse linkalankhula chilankhulo chakechake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amenewo ndipo anagawa zisi za amitundu m'maiko mwao, onse amene monga mwa chinenedwe chao; ndi mwa mabanja ao, ndi m'mitundu yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Amenewa ndiwo makolo a anthu okhala mʼmphepete mwa nyanja. Awa ndi ana a Yafeti monga mwa mafuko a mu mitundu yawo, uliwonse ndi chiyankhulo chake).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amenewo ndipo anagawa zisi za amitundu m'maiko mwao, onse amene monga mwa cinenedwe cao; ndi mwa mabanja ao, ndi m'mitundu yao.