Genesis 10:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Hamu anali Kusi, Ejipito, Libia ndi Kanani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana amuna a Hamu: Kusi, ndi Ejipito, ndi Puti, ndi Kanani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Hamu anali: Kusi, Miziraimu, Puti ndi Kanaani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana amuna a Hamu: Kusi, ndi Mizraimu, ndi Puti, ndi Kanani.