Genesis 10:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kusi adabereka Nimirodi. Nimirodi anali wankhondo woyamba wanyonga pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Kusi anabala Nimirodi; ndipo iye anayamba kukhala wamphamvu pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kusi anabereka Nimurodi amene anali wankhondo wamphamvu kwambiri pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Kusi anabala Nimrode; ndipo iye anayamba kukhala wamphamvu pa dziko lapansi.