Genesis 11:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Poyambayamba anthu onse a pa dziko lapansi ankalankhula chilankhulo chimodzi, ndipo mau amene ankalankhulawo anali amodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo dziko lapansi linali la chinenedwe chimodzi ndi chilankhulidwe chimodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi imeneyo anthu onse a pa dziko lapansi ankayankhula chiyankhulo chimodzi ndipo mawu amene ankayankhula anali amodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo dziko lapansi linali la cinenedwe cimodzi ndi cilankhulidwe cimodzi.