Genesis 11:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Aripakisadi anali wa zaka 35, adabereka mwana dzina lake Sela.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza zisanu nabala Sela;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Aripakisadi anali ndi zaka 35, anabereka Sela.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Aripakasadi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza zisanu, nabala Sela;