Genesis 11:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake adakhala ndi moyo zaka zina 403, ndipo adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza zitatu, atabala Sela, nabala ana aamuna ndi aakazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atabereka Sela, Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka zina 403 ndipo anali ndi ana ena aamuna ndi aakazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo Aripakasadi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza zitatu, atabala Sela, nabala ana amuna ndi akazi.