Genesis 11:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Sela anali wa zaka 30, adabereka mwana dzina lake Eberi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Sela anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Eberi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Sela anali ndi zaka makumi atatu, anabereka Eberi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sela anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Ebere;