Genesis 11:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Eberi ali wa zaka 34, adabereka mwana dzina lake Pelegi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Eberi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza zinai, nabala Pelegi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Eberi anali ndi zaka 34 anabereka Pelegi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Ebere anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza zinai, nabala Pelege;