Genesis 11:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pelegi ali wa zaka 30 adabereka mwana dzina lake Reu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Pelegi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Reu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Pelegi anali ndi zaka makumi atatu, anabereka Reu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Pelege anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala, Reu;