Genesis 11:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atasamukira chakuvuma, adakafika ku chigwa ku dziko la Sinara kumene adakhazikika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali pamene anayendayenda ulendo kum'mawa, anapeza chigwa m'dziko la Sinara, ndipo anakhala kumeneko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene anthu amapita chakummawa anapeza chigwa ku dziko la Sinara nakhazikikako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali pamene anayendayenda ulendo kum'mawa, anapeza cigwa m'dziko la Sinara, ndipo anakhala kumeneko.