Genesis 11:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Reu ali wa zaka 32, adabereka mwana dzina lake Serugi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Reu anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza ziwiri, nabala Serugi:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Reu anali ndi zaka 32, anabereka Serugi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Reu anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza ziwiri, nabala Serugi: