Genesis 11:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Tera adafera kumeneko ali wa zaka 205.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku a Tera anali zaka mazana awiri kudza zisanu; ndipo anafa Tera m'Harani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tera anamwalira ku Harani ali ndi zaka 205.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku a Tera anali zaka mazana awiri kudza zisanu; ndipo anafa Tera m'Harana.