Genesis 11:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Chauta adatsika kudzaona mzindawo, pamodzi ndi nsanja imene anthu ankamanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anatsikira kudzaona mudzi ndi nsanja imene analinkumanga ana a anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehova anatsika kudzaona mzindawo ndi nsanja imene anthu aja ankayimanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anatsikira kudzaona mudzi ndi nsanja imene analinkumanga ana a anthu.