Genesis 13:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyamuka tsopano, uyendere dziko lonselo, chifukwa ndakupatsa,”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tauka, nuyendeyende m'dzikoli m'litali mwake ndi m'mimba mwake; chifukwa kuti ndidzakupatsa iwe limenelo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzuka ndipo uyendere dziko lonseli mulitali ndi mulifupi pakuti ndalipereka kwa iwe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tauka, nuyendeyendc m'dzikoli m'litari mwace ndi m'mimba mwace; cifukwa kuti ndidzakupatsa iwe limenelo.