Genesis 13:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero padaauka ndeu pakati pa abusa a Abramu ndi abusa a Loti. Nthaŵi imeneyo nkuti Akanani ndi Aperizi akadalipo m'dzikomo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali ndeu, abusa a Abramu kudana ndi abusa a Loti: Akanani ndi Aperizi ndipo analinkukhala nthawi yomweyo m'dzikomo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mikangano inayambika pakati pa abusa a Abramu ndi abusa a Loti. Nthawi imeneyo nʼkuti Akanaani ndi Aperezi akukhalanso mʼdziko lomwelo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali ndeu, abusa a Abramu kudana ndi abusa a Loti: Akanani ndi Aperezi ndipo analinkukhala nthawi yomweyo m'dzikomo.