Genesis 14:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamtenganso Loti, mphwake wa Abramu uja, pamodzi ndi zake zonse, chifukwa ankakhala ku Sodomu komweko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anagwira Loti mwana wa Abramu amene anakhala m'Sodomu, ndi chuma chake, namuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anatenganso Loti, mwana wa mʼbale wake wa Abramu pamodzi ndi katundu wake popeza ankakhala mu Sodomu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anagwira Loti mwana wa Abramu amene anakhala m'Sodomu, ndi cuma cace, namuka.