Genesis 14:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
onseŵa adasonkhana kuti athire nkhondo mafumu asanu aŵa: Mfumu Bera wa ku Sodomu, mfumu Birisa wa ku Gomora, mfumu Sinabe wa ku Adima, mfumu Semebera wa ku Zeboimu ndi mfumu ya ku Bela (ndiye kuti Zowari).
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
iwo anathira nkhondo pa Bera mfumu ya Sodomu, ndi pa Birisa, mfumu ya Gomora, ndi pa Sinabe mfumu ya Adima, ndi pa Semebera mfumu ya Zeboimu, ndi pa mfumu ya Bela (kumeneko ndi ku Zowari).
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anathira nkhondo Bera mfumu ya ku Sodomu, Birisa mfumu ya Gomora, Sinabi mfumu ya Adima, Semeberi mfumu ya Ziboimu ndi mfumu ya Bela (kumeneko ndi ku Zowari).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iwo anathira nkhondo pa Bera mfumu ya Sodomu, ndi pa Birisa, mfumu ya Gomora, ndi pa Sinabi mfumu ya Adima, ndi pa Semebere mfumu ya Ziboimu, ndi pa mfumu ya Bela (kumeneko ndi ku Zoari).