Genesis 15:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mtundu umene udzachite zimenezi, ndidzaulanga, ndipo zidzukulu zakozo potuluka m'dzikomo, zidzatenga chuma chambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndiponso mtunduwo adzautumikira, Ine ndidzauweruza: ndiponso pambuyo pake adzatuluka ndi chuma chambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ndidzalanga dziko limene zidzukulu zako zidzagwireko ukapolo ndipo pambuyo pake iwo adzatulukamo ndi chuma chambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndiponso mtunduwo adzautumikira, Ine ndidzauweruza: ndiponso pambuyo pace adzaturuka ndi cuma cambiri.