Genesis 15:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita mibadwo inai, zidzukulu zakozo zidzabwereranso, chifukwa sindidzaŵathamangitsa Aamori mpaka kuipa kwao kutafika pachimake penipeni kuti adzalangidwe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iwo adzabweranso kuno mbadwo wachinai: pakuti mphulupulu za Aamori sizinakwaniridwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patapita mibado inayi, adzukulu ako adzabwereranso kuno popeza tchimo la Aamori silinafike pachimake kuti alangidwe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iwo adzabweranso kuno mbadwo wacinai: pakuti mphulupulu za Aamori sizinakwaniridwe.