Genesis 15:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Abramu adakhulupirira Chauta, ndipo chifukwa cha chimenecho, Chauta adamuwona kuti ndi wolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anakhulupirira Yehova, ndipo kunayesedwa kwa iye chilungamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abramu anakhulupirira Yehova, ndipo ichi chinamuchititsa kukhala wolungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anakhulupirira Yehova, ndipo kunayesedwa kwa iye cilungamo.