Genesis 16:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sarai mkazi wa Abramu, sadam'balire ana Abramuyo. Koma Sarai anali ndi mdzakazi wake wa ku Ejipito dzina lake Hagara.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Sarai mkazi wake wa Abramu sanambalire iye mwana; ndipo anali ndi mdzakazi, wa ku Ejipito, dzina lake Hagara.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Sarai, mkazi wa Abramu anali asanamuberekere ana Abramuyo. Koma anali ndi wantchito wamkazi wa ku Igupto dzina lake Hagara;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sarai mkazi wace wa Abramu sanambalire iye mwana; ndipo anali ndi mdzakazi, wa ku Aigupto, dzina lace Hagara.