Genesis 16:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Hagara adamubalira Abramu mwana wamwamuna, namutcha dzina loti Ismaele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Hagara anambalira Abramu mwana wamwamuna ndipo Abramu anatcha dzina la mwana wake amene anambalira iye Hagara, Ismaele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Hagara anamuberekera Abramu mwana wamwamuna ndipo Abramu anamutcha mwanayo Ismaeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Hagara anambalira Abramumwana wamwamuna, ndipo Abramu anacha dzina la mwana wace amene anambalira iye Hagara, lsmayeli.