Genesis 17:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzachita nawe chipangano, ndipo ndidzakupatsa zidzukulu zambiri.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzapangana pangano langa ndi Ine ndi iwe, ndipo ndidzachulukitsa iwe kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Ine ndikulonjeza kuti ndidzakupatsa zidzukulu zambiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzapangana pangano langa ndi Ine ndi iwe, ndipo ndidzacurukitsa iwe kwambiri.