Genesis 17:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abrahamu anali wa zaka 99 pa nthaŵi imene adaumbalidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Abrahamu anali wa zaka makumi asanu ndi anai kudza zisanu ndi zinai, pamene anadulidwa m'khungu lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abrahamu anali ndi zaka 99 pamene anachita mdulidwe,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Abrahamu anali wa zaka makumi asanu ndi anai kudza zisanu ndi zinai, pamene anadulidwa m'khungu lace.