Genesis 17:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wake Ismaele anali wa zaka 13 pamene adaumbalidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ismaele mwana wake anali wa zaka khumi ndi zitatu pamene anadulidwa m'khungu lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo mwana wake Ismaeli anali ndi zaka khumi ndi zitatu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Ismayeli mwana wace anali wa zaka khumi ndi zitatu pamene anadulidwa m'khungu lace.