Genesis 18:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
nati, “Mbuyanga, ngati ndapeza kuyanja pamaso panu, chonde musapitirire pakhomo pa mtumiki wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mbuyanga, ngatitu ndi ndikapeza ufulu pamaso panu, musapitiriretu pa kapolo wanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati mwandikomera mtima, mbuye wanga, musamulambalale mtumiki wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mbuyanga, ngatitu ndikapeza ufulu pamaso panu, musapitiriretu pa kapolo wanu;