Genesis 18:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adatenga chambiko ndi mkaka wokama chatsopano, ndi nyama yokonzakonza ija naŵapatsa zonsezo. Iye adakhala potero pamene anthuwo analikudya patsinde pa mtengo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatenga mafuta amkaka, ndi mkaka, ndi kamwana ka ng'ombe kamene anaphika, naziika patsogolo pao; ndipo iye anaimirira iwo patsinde pa mtengo, ndipo anadya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Abrahamu anatenga chambiko, mkaka ndi mwana wangʼombe wokonzedwa uja nazipereka kwa anthu aja. Alendowo akudya, Abrahamu ankawayangʼana atayimirira pansi pa mtengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatenga mafuta amkaka, ndi mkaka, ndi kamwana ka ng'ombe kamene anaphika, naziika patsogolo pao; ndipo iye anaimirira iwo patsinde pa mtengo, ndipo anadya.