Genesis 19:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu aŵiri anali m'kati aja adamkokera Lotiyo m'nyumba, natseka chitseko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anthu aja anatulutsa dzanja lao, namlowetsa Loti momwe anali iwo m'nyumba, natseka pakhomo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu aja anali mʼkatiwa anasuzumira namukokera Loti uja mʼkati mwa nyumba nʼkutseka chitseko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Komo anthu aja anaturutsa dzanja lao, namlowetsa Loti momwe anali iwo m'nyumba, natseka pakhomo,