Genesis 19:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
chifukwa ife tikuti tiwononge malo ano. Chauta waziona zoipa zonse zimene anthu okhala mumzinda muno akuchita, ndipo tatumidwa kuti tiuwononge mzindawu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
popeza ife tidzaononga malo ano, chifukwa kulira kwao kwakula pamaso pa Yehova, ndipo Yehova anatitumiza ife kuti tiuononge.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa tiwononga malo ano. Yehova waona kuti kuyipa kwa anthu a mu mzindawu kwakulitsa. Choncho watituma kuti tiwuwononge.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
popeza ife tidzaononga malo ano, cifukwa kulira kwao kwakula pamaso pa Yehova, ndipo Yehova anatitumiza ife kuti tiuononge.