Genesis 19:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero adaonongeratu mizinda imeneyi, pamodzi ndi chigwa chonse ndi anthu onse am'mizindamo, kuphatikizapo zomera zonse za m'dziko limenelo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anaononga midziyo, ndi chigwa chonse, ndi onse akukhala m'midzimo, ndi zimene zimera panthaka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero, anawononga mizindayo, chigwa chonse pamodzi ndi onse okhala mʼmizindayo. Anawononganso zomera zonse za mʼdzikolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anaononga midziyo, ndi cigwa conse, ndi onse akukhala m'midzimo, ndi zimene zimera panthaka.