Genesis 19:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wamkuluyo adabala mwana wamwamuna, namutcha Mowabu. Iyeyo ndiye kholo la Amowabu onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Woyamba ndipo anabala mwana wamwamuna, namtcha dzina lake. Mowabu; yemweyo ndi atate wa Amowabu kufikira lero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wamkazi wamkulu uja anabereka mwana wa mwamuna ndipo anamutcha Mowabu. Iyeyo ndiye kholo la Amowabu onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Woyamba ndipo anabala mwana wamwamona, namcha dzina lace. Moabu; yemweyo ndi atate wa Amoabu kufikira lero.