Genesis 19:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wamng'onoyo nayenso adabala mwana wamwamuna, namutcha Benami. Iyeyo ndiye kholo la Aamoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wamng'ono ndipo anabala mwana wamwamuna, namtcha dzina lake Benami; yemweyo ndi atate wa Aamoni kufikira lero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wamkazi wamngʼono naye anabereka mwana wamwamuna, ndipo anamutcha iye Beni-Ammi. Iyeyu ndiye kholo la Aamoni onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wamng'ono ndipo anabala mwana wamwamuna, namcha dzina lace Benammi; yemweyo ndi atate wa Aamoni kufikira lero.