Genesis 2:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma madzi ankatuluka m'dziko lonse lapansi ndi kumathirira nthaka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma inakwera nkhungu yotuluka pa dziko lapansi, niithirira ponse pamwamba pa nthaka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma kasupe ankatuluka mʼnthaka ndi kuthirira pa dziko lonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kama inakwera nkhungu yoturuka pa dziko lapansi, niithirira ponse pamwamba pa nthaka.