Genesis 21:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zidamuvuta kwambiri Abrahamu, chifukwa chakuti Ismaele nayenso anali mwana wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mauwo anaipira Abrahamu chifukwa cha mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nkhaniyi inamumvetsa chisoni kwambiri Abrahamu chifukwa imakhudza mwana wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mauwo anaipira Abrahamu cifukwa ca mwana wace.