Genesis 21:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono madzi aja atamthera, adangosiya mwanayo pa chitsamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatha madzi a m'mchenje ndipo anaika mwana pansi pa chitsamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Madzi atatha mʼbotolo muja, anamuyika mnyamatayo pansi pa zitsamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatha madzi a m'mcenje ndipo anaika mwana pansi pa citsamba.