Genesis 21:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake tsono, lumbirani pano pamaso pa Mulungu kuti simudzandinyenga ineyo, kapena ana anga, kapenanso zidzukulu zanga. Ine ndakhala wokhulupirika kwa inu, ndiye inunso mulonjeze kuti mudzakhala wokhulupirika kwa ine, m'dziko limene mukukhalamolo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
tsopano iwe undilumbirire ine pano pa Mulungu kuti sudzandinyenga ine, kapena mwana wanga, kapena mdzukulu wanga: koma monga ufulu ndakuchitira iwe udzandichitire ine, ndi dziko lomwe wakhalamo, ngati mlendo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano undilumbirire ine pano pamaso pa Mulungu kuti sudzachita mwa chinyengo ndi ine kapena ana anga kapena zidzukulu zanga. Undionetse ine pamodzi ndi dziko limene ukukhalamo ngati mlendo, kukoma mtima kokhala ngati kumene ndinakuonetsa ine.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
tsopano iwe undilumbirire ine pano pa Mulungu kuti sudzandinyenga ine, kapena mwana wanga, kapena mdzukulu wanga: koma monga ufulu ndakucitira iwe udzandicitire ine, ndi dziko lomwe wakhalamo, ngati mlendo.